×
Home Files Nkhani MisonkhanoZitsanzoToolsAbout

Mfundo zobwereza:
Kodi Ndingatani Ngati Ndaphwanya Lamulo la Makolo Anga?

  • Muzivomereza zimene mwalakwitsa.

    Makolo anu amadziwa kuti si inu wangwiro. Koma funso n'kumati, Kodi ndinu woona mtima?
  • Muzipepesa.

    Muzinena kuti “pepani” ndipo muzipewa kupereka zifukwa zodzikhululukira.
  • Muzivomereza chilango chimene mwalandira.

    Muzichita zinthu mogwirizana ndi chilango chimene makolo angakupatseni.
  • Muziyesetsa kukhala wodalirika.

    Muyambe kuchita zinthu zimene zingasonyeze kuti ndinu wodalirika.


  • Back to top

    “M'patseni Yehova ulemelero
    woyenera dzina lake.”
       - Salimo 96:8.